Lesson 3 for July 18 2020 Kutsogolera Ena Kulandira Aliyense Kupanga Maubwenzi Kuchitira ena za bwino Kugwiritsa Ntchito Mwai Uliwonse Kodi Yesu ankaona ID: 815178
Download The PPT/PDF document "KUONA ANTHU KUPYOLERA MMASO A YESU" is the property of its rightful owner. Permission is granted to download and print the materials on this web site for personal, non-commercial use only, and to display it on your personal computer provided you do not modify the materials and that you retain all copyright notices contained in the materials. By downloading content from our website, you accept the terms of this agreement.
Slide1
KUONA ANTHU KUPYOLERA MMASO A YESU
Lesson 3 for July 18, 2020
Slide2Kutsogolera
Ena
Kulandira AliyenseKupanga MaubwenziKuchitira ena za bwinoKugwiritsa Ntchito Mwai Uliwonse
Kodi Yesu ankaona anthu motani?Ankawachitira chifundo. Ankaganizira kuti moyo uli wonse tiofunika kupulumuka. Ankaona munthu mmene angasinthira atalandira chipulumutso.Munthu aliye anali wafunika ndi wapadera kwa Yesu. Kotero, samanyoza aliyense koma ankamuona aliyense mwa njira yapadera. Tiyeni tiphunzire kuona anzathu mmene Yesu akanawaonera.
Slide3KUTSOGOLERA ENA
“
Ndipo
anadza ku Betsaida. Ndipo anadza naye kwa Iye munthu wakhungu, nampempha Iye kuti amkhudze.”
(Marko 8:22)Ichi chinali chozizwitsa chapadera m’njira za mbiri.
1. Anthu ena, anabwera
ndi nzawo wakhungu, napempha kuti
Yesu amuchize
2. Yesu anamutengera
pambali
3.
Atamukhudza
koyamba
,
anamufunsa
ngati
akuona
kanthu
4.
Wakhunguyu anaona anthu ngati mitengo
5. Atakhudzidwa kachiwiri, anachira kwathuthu
Slide4KULANDIRA ALIYENSE
“
Ndipo
anayenera kupita pakati pa Samariya.” (Yohane 4:4)Ubale wapakati pa a Yuda ndi a Samaliya unali oteketseka. Ayuda pochoka ku Yudea kupita ku Galileya ankazungulira mzinda
wa Samaliya posafunina kudutsamo.GalileyaSamaliyaYudeaPamene tiona ena ndi chifundo cha Mulungu, matchinga onse amaphwasulidwa
. Sipakhalanso kusiyana, chifukwa aliyense timamuona oyenera kulowa mu ufumu wa
kumwambaSitikuyera kugwirizana nawo
mmaganizo awo a ndale kapena chipembedzo
, Koma timawakonda ndipo timawafunira zabwino
.
Koma
,
Yesu
amaona
kupyola
,
mtundu
,
chikhalidwe
,
chibadidwe
komanso chipembedzo. Ankadziwa kuti ku
Samaliyanso kunali anthu ofunika chipulumutso,ndipo inali ntchito yake kuwapititsira chipulumutso.
Slide5KUPANGA MA UBWENZI
“
Anayamba
iye kupeza mbale wake yekha Simoni, nanena naye, Tapeza ife Mesiya (ndiko kusandulika Khristu).”
(Yohane 1:41)Pamene Yesu ankatsanzika ophunzira ake, anawapempha alalikira uthenga wabwino kumadera ambiri: “Ku Yerusalemu, konse ku Yudea ndi Samaliya, ndi kumapeto a dziko.” (Machitidwe 1:8).
Ntumwi Andrea anapereka
chitsanzo chabwino. Koyamba, Anauza nchimwene
wake za Yesu[Yudea].Kenaka anapanga
ubwenzi ndi ka nyamata[Samaliya] nachita
zozizwa kuopyolera mwa iye (
Yohane
6:5-11).
Pambuyo
pake
anagawa
uthenga
wabwino
kwa
alendo [kumapeto a dziko], monga a Giriki amene ankafuna kudziwa za
Yesu(Yohane 12:20-26).Tingathe kuphunzira kagwiridwe ka ntchito
yokopa anthu kuchokora kwa Andrea: Kupanga ma ubwenzi
/ubale ndi ena.
Slide6KUCHITIRA ENA ZABWINO
“
Ndipo
pakuona kuti anayankha ndi nzeru, Yesu anati kwa iye, Suli kutali ndi
Ufumu wa Mulungu. Ndipo palibe munthu analimbanso mtima kumfunsa Iye kanthu.” (Marko 12:34)Kodi Yesu
anachita nawo bwanji anthu ovuta?
Kuona
anthu ena
m’maso a Yesu zikutathauza kuona ena
kuti ndi mbadwa za ufumu wa
kumwamba,ndi
kuchita
nawo
moyenera
.
Kuti
tipindule
ndi umboni
wathu, tikuyenera kupempha Mzimu Woyera ativumbulutsire chinsinsi ichi.
Slide7KUGWIRITSA NTCHITO MWAI ONSE OPEZEKA
“
Ndidziwa
ntchito zako (taona, ndapatsa pamaso pako khomo lotseguka limene munthu sangathe kutsekapo), kuti uli nayo
mphamvu pang'ono, ndipo unasunga mau anga, osakana dzina langa.” (Chivumbulutso 3:8)Mulungu amatsegula makomo kutipatsa mwai oti
tiperekere umboni.Mwachitsanzo Filipi: Mulungu anamuika pa malo
oti akumane ndi munthu yemwe
ankawerenga malemba a nchipangano chakale. Munthuyu
ankangofunika kuthandizidwa pangóno kuti apereke
moyo wake kwa Yesu(Acts 8:26-39).Pali
angelo
osaoneka
ndi
maso
anthu
omwe
ndiokozeka kutionetsa
iwo amene angatsegule makomo awo kulandira mawo a Mulungu. Pemphani Mulungu akupatseni
masomphenya ozindikira mwai opezeka komanso mawo oyenera kugawana ndi ena
Slide8“Yesu anakhala yekha
pakati
pa anthu. Sanazipatule kwa iwo amene anafuna chithandizo kuchokera kwa iye. Analowa nyumba za anthu, ku khudza olira, kuchidza odwala, kudzudzula olakwitsa, ndi
kuchita ntchito za bwino. Ndipo ngati tikutsata mapazi a Yesu, tichite momwe anachitira iye. Tithandize ena monga mmene iye anachitira.”E.G.W. (Our Father Cares, February 17)