/
“ Taonani ,  Mulungu “ Taonani ,  Mulungu

“ Taonani , Mulungu - PowerPoint Presentation

studmonkeybikers
studmonkeybikers . @studmonkeybikers
Follow
342 views
Uploaded On 2020-10-22

“ Taonani , Mulungu - PPT Presentation

achita mokwezeka mu mphamvu yake mphunzitsi wakunga Iye ndani Jobu 3622 Mwananga tamva mwambo wa atate wako ndi kusasiya ID: 815702

ndipo mulungu cha kwa mulungu ndipo kwa cha ndi iye ulemerero yehova inu munthu mphamvu akorinto chifukwa sabata wanu

Share:

Link:

Embed:

Download Presentation from below link

Download The PPT/PDF document "“ Taonani , Mulungu" is the property of its rightful owner. Permission is granted to download and print the materials on this web site for personal, non-commercial use only, and to display it on your personal computer provided you do not modify the materials and that you retain all copyright notices contained in the materials. By downloading content from our website, you accept the terms of this agreement.


Presentation Transcript

Slide1

Taonani

,

Mulungu

achita

mokwezeka

mu

mphamvu

yake

,

mphunzitsi

wakunga

Iye

ndani

,

?”

(

Jobu

36:22)

Slide2

Mwananga

,

tamva

mwambo

wa

atate

wako

,

ndi

kusasiya

chilangizo

cha

amai

ako

(

Miyambo

1:8)

Slide3

Ndipi

muzikonda Yehova Mulungu wanu

ndi mtima

wanu

wonse

,

ndi

moyo

wanu

wonse

,

ndi

mphamvu

yanu

yonse

(

Deuteronomo

6:5)

Slide4

Maso

a Yehova

ali

ponseponse

,

nayang'anira

oipa

ndi

abwino

.

(

Miyambo

15:3)

Slide5

Pakuti

Mulungu

amene

anati

,

Kuunika

kudzawala

kutuluka

mumdima

,

ndiye

amene

anawala

m’mitima

yathu

kutipatsa

chiwalitsiro

cha

chidziwitso

cha

ulemerero

wa

Mulungu

pankhope

ya

Yesu

Khristu

(2

Akorinto

4:6)

Slide6

Ndipo

Yesu anati kwa iye

, Muka; chikhulupiriro

chako

chakupulumutsa

iwe

.

Ndipo

pomwepo

anapenyanso

;

namtsata

Iye

panjira

(Mark 10:52)

Slide7

Mchitireni

Yehova

ulemerero

wa

dzina

lake;

bwerani

nacho

chopereka

,

ndipo fikani pamaso pake; lambirani Yehova m'chiyero chokometsetsa.”(1 Mbiri 16:29)

Slide8

Lemba

lililonse adaliuzira Mulungu, ndipo

lipindulitsa pa chiphunzitso,

chitsutsano

,

chikonzero

,

chilangizo

cha

m'chilungamo

”(2 Timoteo 3:16)

Slide9

K

apena

sitinakhala

ofuna

ulemerero

wa

kwa anthu, kapena kwa inu, kapena kwa ena

, tingakhale tinali nayo mphamvu yakukulemetsani monga

atumwi a Khristu. Komatu tinakhala ofatsa pakati

pa inu, monga

m'mene mlezi afukata ana ake a iye yekha. kotero ife poliralira inu, tinavomera mokondwera kupereka kwa inu si Uthenga Wabwino wa Mulungu wokha, komanso moyo wathu, popeza mudakhala okondedwa kwa ife.”(1 Atesalonika 2:5-9)

Slide10

Zakumwamba

zimalalikira ulemerero wa

Mulungu;

ndipo

nthambo

lionetsa

ntchito

ya manja ake”(Masalimo 19:1)

Slide11

Chifukwa

chake

abale anga

okondedwa

,

khalani

okhazikika

,

osasunthika, akuchuluka mu ntchito ya Ambuye, nthawi

zones, podziwa kuti kuchititsa kwanu

Sikuli chabe mwa Ambuye.”

(1 Akorinto 15:58)

Slide12

Ndipo

ananena

nao,

Sabata

linaikidwa

chifukwa

cha

munthu

, si munthu

chifukwa cha Sabata. motero

Mwana wa

Munthu

ali mwini tsiku la Sabata lomwe’ ” (Marko 2:27-28)

Slide13

koma monga kwalembedwa, Zimene

diso silinaziona,

ndi

khutu

silinazimva

,

nisizinalowa

mu mtima wa munthu, zimene zilizonse Mulungu anakonzereratu iwo

akumkonda Iye’ ”(1 Akorinto 2:9)

Related Contents


Next Show more